Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+

  • Genesis 19:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiyeno alendowo anafunsa Loti kuti: “Kodi uli ndi achibale alionse kuno? Uwatulutse mumzinda uno,+ kaya ndi akamwini ako, ana ako aamuna, ana ako aakazi, kapena alionse amene ndi abale ako.

  • Numeri 16:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Atafika anauza khamulo kuti: “Chonde, chokani kumahema a anthu oipawa, ndipo musakhudze chinthu chawo chilichonse,+ kuti musaphedwe nawo limodzi chifukwa cha kuchimwa kwawo.”

  • 1 Mafumu 20:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiyeno atumiki ake anamuuza kuti: “Tamva kuti mafumu a nyumba ya Isiraeli ndiwo mafumu amene amasonyeza kukoma mtima kosatha.+ Tiyeni tivale ziguduli*+ m’chiuno mwathu+ ndi kumanga zingwe kumutu kwathu, kuti tipite kwa mfumu ya Isiraeli. Mwina sikakuphani.”+

  • Miyambo 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi zimateteza mfumu,+ ndipo chifukwa cha kukoma mtima kosatha kumeneko mfumu imakhazikitsa mpando wake wachifumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena