Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 37:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+

  • 1 Mafumu 21:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ahabu atangomva mawu amenewa, anang’amba zovala zake n’kuvala chiguduli.+ Iye anayamba kusala kudya, kugona pachiguduli ndipo anali kuyenda mwachisoni.+

  • Esitere 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Moredekai+ anadziwa zonse zimene zinachitika.+ Choncho anang’amba zovala zake ndi kuvala chiguduli*+ ndipo anadzithira phulusa+ ndi kutuluka kupita pakati pa mzinda. Ndiyeno anayamba kulira mofuula ndiponso mopwetekedwa mtima.+

  • Yesaya 22:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ adzalamula anthu kuti alire,+ agwetse misozi, amete mipala ndiponso avale ziguduli m’chiuno.+

  • Chivumbulutso 11:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno ndidzachititsa mboni zanga ziwiri+ kunenera+ kwa masiku 1,260, zitavala ziguduli.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena