Salimo 61:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mfumuyo idzakhala pamaso pa Mulungu mpaka kalekale.+Isonyezeni kukoma mtima kwanu kosatha ndi kuipatsa choonadi kuti zimenezi ziiteteze.+ Miyambo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Cholakwa chimaphimbika ndi kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi,+ ndipo chifukwa choopa Yehova munthu amapatuka pa choipa.+
7 Mfumuyo idzakhala pamaso pa Mulungu mpaka kalekale.+Isonyezeni kukoma mtima kwanu kosatha ndi kuipatsa choonadi kuti zimenezi ziiteteze.+
6 Cholakwa chimaphimbika ndi kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi,+ ndipo chifukwa choopa Yehova munthu amapatuka pa choipa.+