2 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ Salimo 41:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma ine mwandichirikiza chifukwa cha mtima wanga wosagawanika,+Ndipo mudzandiika pamaso panu mpaka kalekale.+
16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+
12 Koma ine mwandichirikiza chifukwa cha mtima wanga wosagawanika,+Ndipo mudzandiika pamaso panu mpaka kalekale.+