Yobu 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Kudziko la Uzi+ kunali munthu wina dzina lake Yobu.+ Iye anali munthu wopanda cholakwa,+ wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndiponso wopewa zoipa.+ Salimo 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtima wanga wosagawanika ndiponso wowongoka unditeteze,+Pakuti chiyembekezo changa chili mwa inu.+ Miyambo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu owongoka mtima, iye amawasungira nzeru zopindulitsa.+ Kwa anthu oyenda ndi mtima wosagawanika, iye amakhala chishango+ Miyambo 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Njira ya Yehova ndiyo malo achitetezo kwa munthu wopanda cholakwa,+ koma anthu ochita zopweteka ena adzawonongedwa.+
1 Kudziko la Uzi+ kunali munthu wina dzina lake Yobu.+ Iye anali munthu wopanda cholakwa,+ wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndiponso wopewa zoipa.+
21 Mtima wanga wosagawanika ndiponso wowongoka unditeteze,+Pakuti chiyembekezo changa chili mwa inu.+
7 Anthu owongoka mtima, iye amawasungira nzeru zopindulitsa.+ Kwa anthu oyenda ndi mtima wosagawanika, iye amakhala chishango+
29 Njira ya Yehova ndiyo malo achitetezo kwa munthu wopanda cholakwa,+ koma anthu ochita zopweteka ena adzawonongedwa.+