Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+ Salimo 140:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithudi, anthu olungama adzatamanda dzina lanu.+Anthu owongoka mtima adzakhalabe pamaso panu.+