Salimo 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, musasiye kundimvera chisoni.+Kukoma mtima kwanu kosatha komanso choonadi chanu zinditeteze nthawi zonse.+ Salimo 57:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Adzatumiza thandizo kuchokera kumwamba ndi kundipulumutsa.+Adzasokoneza wofuna kundiwakha ndi pakamwa pake.+ [Seʹlah.]Mulungu adzasonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndi choonadi chake.+ Salimo 143:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Adani anga muwakhalitse chete monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndipo muwononge onse ondichitira zoipa,+Pakuti ine ndine mtumiki wanu.+ Miyambo 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi zimateteza mfumu,+ ndipo chifukwa cha kukoma mtima kosatha kumeneko mfumu imakhazikitsa mpando wake wachifumu.+ Mika 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zonse zimene munanena kwa Yakobo zinali zoona ndipo Abulahamu munamusonyeza kukoma mtima kosatha. Ifenso mudzatichitira zomwezo chifukwa n’zimene munalonjeza makolo athu kalekale.+
11 Inu Yehova, musasiye kundimvera chisoni.+Kukoma mtima kwanu kosatha komanso choonadi chanu zinditeteze nthawi zonse.+
3 Adzatumiza thandizo kuchokera kumwamba ndi kundipulumutsa.+Adzasokoneza wofuna kundiwakha ndi pakamwa pake.+ [Seʹlah.]Mulungu adzasonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndi choonadi chake.+
12 Adani anga muwakhalitse chete monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Ndipo muwononge onse ondichitira zoipa,+Pakuti ine ndine mtumiki wanu.+
28 Kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi zimateteza mfumu,+ ndipo chifukwa cha kukoma mtima kosatha kumeneko mfumu imakhazikitsa mpando wake wachifumu.+
20 Zonse zimene munanena kwa Yakobo zinali zoona ndipo Abulahamu munamusonyeza kukoma mtima kosatha. Ifenso mudzatichitira zomwezo chifukwa n’zimene munalonjeza makolo athu kalekale.+