Salimo 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, musasiye kundimvera chisoni.+Kukoma mtima kwanu kosatha komanso choonadi chanu zinditeteze nthawi zonse.+ Salimo 61:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mfumuyo idzakhala pamaso pa Mulungu mpaka kalekale.+Isonyezeni kukoma mtima kwanu kosatha ndi kuipatsa choonadi kuti zimenezi ziiteteze.+ Yohane 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Popeza Chilamulo chinaperekedwa kudzera mwa Mose,+ kukoma mtima kwakukulu+ komanso choonadi+ zinakhalako kudzera mwa Yesu Khristu.
11 Inu Yehova, musasiye kundimvera chisoni.+Kukoma mtima kwanu kosatha komanso choonadi chanu zinditeteze nthawi zonse.+
7 Mfumuyo idzakhala pamaso pa Mulungu mpaka kalekale.+Isonyezeni kukoma mtima kwanu kosatha ndi kuipatsa choonadi kuti zimenezi ziiteteze.+
17 Popeza Chilamulo chinaperekedwa kudzera mwa Mose,+ kukoma mtima kwakukulu+ komanso choonadi+ zinakhalako kudzera mwa Yesu Khristu.