Salimo 57:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Adzatumiza thandizo kuchokera kumwamba nʼkundipulumutsa.+ Adzasokoneza wofuna kundiwakha ndi pakamwa pake. (Selah) Mulungu adzasonyeza chikondi chake chokhulupirika ndi choonadi chake.+
3 Adzatumiza thandizo kuchokera kumwamba nʼkundipulumutsa.+ Adzasokoneza wofuna kundiwakha ndi pakamwa pake. (Selah) Mulungu adzasonyeza chikondi chake chokhulupirika ndi choonadi chake.+