Numeri 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atafika anauza khamulo kuti: “Chonde, chokani kumahema a anthu oipawa, ndipo musakhudze chinthu chawo chilichonse,+ kuti musaphedwe nawo limodzi chifukwa cha kuchimwa kwawo.” 1 Samueli 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zili choncho, Sauli anauza Akeni+ kuti: “Nyamukani,+ muchoke pakati pa Aamaleki kuti ndisakuwonongeni pamodzi nawo. Inuyo munasonyeza kukoma mtima kosatha kwa ana onse a Isiraeli+ atatuluka mu Iguputo.”+ Choncho Akeni anachokadi pakati pa Aamaleki. Yeremiya 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Thawani ndi kutuluka m’Babulo+ ndipo aliyense apulumutse moyo wake.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake.+ Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere chilango.+ Mulungu abwezera Babulo mogwirizana ndi zochita zake.+
26 Atafika anauza khamulo kuti: “Chonde, chokani kumahema a anthu oipawa, ndipo musakhudze chinthu chawo chilichonse,+ kuti musaphedwe nawo limodzi chifukwa cha kuchimwa kwawo.”
6 Zili choncho, Sauli anauza Akeni+ kuti: “Nyamukani,+ muchoke pakati pa Aamaleki kuti ndisakuwonongeni pamodzi nawo. Inuyo munasonyeza kukoma mtima kosatha kwa ana onse a Isiraeli+ atatuluka mu Iguputo.”+ Choncho Akeni anachokadi pakati pa Aamaleki.
6 “Thawani ndi kutuluka m’Babulo+ ndipo aliyense apulumutse moyo wake.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake.+ Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere chilango.+ Mulungu abwezera Babulo mogwirizana ndi zochita zake.+