Yeremiya 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Thawani m’Babulo ndipo tulukani m’dziko la Akasidi.+ Mukhale ngati mbuzi zamphongo ndi nkhosa zamphongo zimene zikutsogolera gulu lonse.+ Chivumbulutso 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.
8 “Thawani m’Babulo ndipo tulukani m’dziko la Akasidi.+ Mukhale ngati mbuzi zamphongo ndi nkhosa zamphongo zimene zikutsogolera gulu lonse.+
4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.