Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 48:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tulukani m’Babulo anthu inu!+ Thawani m’manja mwa Akasidi.+ Nenani zimenezi ndi mfuu yachisangalalo kuti zimveke.+ Zineneni mokuwa mpaka zimveke kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+

  • Yesaya 52:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tembenukani! Tembenukani! Tulukani mmenemo!+ Musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa.+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera, inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+

  • Yeremiya 50:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Thawani m’Babulo ndipo tulukani m’dziko la Akasidi.+ Mukhale ngati mbuzi zamphongo ndi nkhosa zamphongo zimene zikutsogolera gulu lonse.+

  • Yeremiya 51:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ndipo aliyense wa inu apulumutse moyo wake+ ku mkwiyo wa Yehova woyaka moto.+

  • Zekariya 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Fulumira Ziyoni!+ Thawa, iwe amene ukukhala ndi mwana wamkazi wa Babulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena