Genesis 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Atafika nawo kunja kwa mzinda, mmodzi wa iwo anati: “Thawani mupulumutse moyo wanu!+ Musacheukire kumbuyo+ ndipo musaime chilili pamalo alionse m’Chigawochi.*+ Thawirani kudera la kumapiri kuti musawonongedwe!”+ Yeremiya 51:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Thawani ndi kutuluka m’Babulo+ ndipo aliyense apulumutse moyo wake.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake.+ Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere chilango.+ Mulungu abwezera Babulo mogwirizana ndi zochita zake.+ Zekariya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Fulumira Ziyoni!+ Thawa, iwe amene ukukhala ndi mwana wamkazi wa Babulo.+
17 Atafika nawo kunja kwa mzinda, mmodzi wa iwo anati: “Thawani mupulumutse moyo wanu!+ Musacheukire kumbuyo+ ndipo musaime chilili pamalo alionse m’Chigawochi.*+ Thawirani kudera la kumapiri kuti musawonongedwe!”+
6 “Thawani ndi kutuluka m’Babulo+ ndipo aliyense apulumutse moyo wake.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake.+ Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere chilango.+ Mulungu abwezera Babulo mogwirizana ndi zochita zake.+