Mateyu 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 amene ali mu Yudeya adzayambe kuthawira+ kumapiri. Aheberi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 tidzapulumuka bwanji+ ngati tanyalanyaza+ chipulumutso chachikulu chonchi?+ Ambuye wathu ndi amene anayamba kunena za chipulumutso chimenechi,+ ndipo anthu amene anamumva anatitsimikizira zimenezo.+
3 tidzapulumuka bwanji+ ngati tanyalanyaza+ chipulumutso chachikulu chonchi?+ Ambuye wathu ndi amene anayamba kunena za chipulumutso chimenechi,+ ndipo anthu amene anamumva anatitsimikizira zimenezo.+