Aheberi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndiye tidzapulumuka bwanji ngati titanyalanyaza chipulumutso chachikulu chonchi?+ Ambuye wathu ndi amene anayamba kunena za chipulumutsochi+ ndipo anthu amene anamumva anatitsimikizira zimenezo. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:3 Nsanja ya Olonda,5/1/1990, tsa. 30
3 ndiye tidzapulumuka bwanji ngati titanyalanyaza chipulumutso chachikulu chonchi?+ Ambuye wathu ndi amene anayamba kunena za chipulumutsochi+ ndipo anthu amene anamumva anatitsimikizira zimenezo.