Genesis 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako, mkazi wake amene anali kumbuyo kwake anacheukira kumbuyo, ndipo anasanduka chipilala chamchere.+ Numeri 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atafika anauza khamulo kuti: “Chonde, chokani kumahema a anthu oipawa, ndipo musakhudze chinthu chawo chilichonse,+ kuti musaphedwe nawo limodzi chifukwa cha kuchimwa kwawo.”
26 Kenako, mkazi wake amene anali kumbuyo kwake anacheukira kumbuyo, ndipo anasanduka chipilala chamchere.+
26 Atafika anauza khamulo kuti: “Chonde, chokani kumahema a anthu oipawa, ndipo musakhudze chinthu chawo chilichonse,+ kuti musaphedwe nawo limodzi chifukwa cha kuchimwa kwawo.”