Yeremiya 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti mitundu yambiri ndi mafumu otchuka+ agwiritsa ntchito anthu anga monga antchito awo.+ Chotero ndidzawabwezera mogwirizana ndi zochita zawo ndiponso mogwirizana ndi ntchito za manja awo.’”+
14 Pakuti mitundu yambiri ndi mafumu otchuka+ agwiritsa ntchito anthu anga monga antchito awo.+ Chotero ndidzawabwezera mogwirizana ndi zochita zawo ndiponso mogwirizana ndi ntchito za manja awo.’”+