Salimo 90:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndani angadziwe kukula kwa ukali wanu,+Ndi kukula kwa mkwiyo wanu kumene kumafanana ndi ulemu umene muyenera kulandira?+ Yesaya 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa cha zimenezi, ndidzachititsa kuti kumwamba kugwedezeke+ ndipo dziko lapansi lidzanjenjemera n’kuchoka m’malo mwake, chifukwa cha ukali wa Yehova wa makamu,+ pa tsiku limene mkwiyo wake udzayake.+
11 Ndani angadziwe kukula kwa ukali wanu,+Ndi kukula kwa mkwiyo wanu kumene kumafanana ndi ulemu umene muyenera kulandira?+
13 Chifukwa cha zimenezi, ndidzachititsa kuti kumwamba kugwedezeke+ ndipo dziko lapansi lidzanjenjemera n’kuchoka m’malo mwake, chifukwa cha ukali wa Yehova wa makamu,+ pa tsiku limene mkwiyo wake udzayake.+