Yesaya 33:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mu Ziyoni, anthu ochimwa akuchita mantha.+ Opanduka akunjenjemera kwambiri.+ Akufunsa kuti: ‘Ndani wa ife angakhale pambali pa moto wowononga?+ Ndani wa ife angakhale pafupi ndi moto woyaka kwambiri wosatherapo?’+ Luka 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ndikuuzani woti muzimuopa: Muziopa iye+ amene amati akapha, amakhalanso ndi mphamvu zoponya munthu m’Gehena.*+ Ndithu ndikukuuzani, muziopa+ Ameneyu.
14 Mu Ziyoni, anthu ochimwa akuchita mantha.+ Opanduka akunjenjemera kwambiri.+ Akufunsa kuti: ‘Ndani wa ife angakhale pambali pa moto wowononga?+ Ndani wa ife angakhale pafupi ndi moto woyaka kwambiri wosatherapo?’+
5 Koma ndikuuzani woti muzimuopa: Muziopa iye+ amene amati akapha, amakhalanso ndi mphamvu zoponya munthu m’Gehena.*+ Ndithu ndikukuuzani, muziopa+ Ameneyu.