Luka 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ndikuuzani woti muzimuopa: Muziopa Iye amene amati akapha, amakhalanso ndi mphamvu zoponya munthu mʼGehena.*+ Ndithu ndikukuuzani, muziopa Ameneyu.+
5 Koma ndikuuzani woti muzimuopa: Muziopa Iye amene amati akapha, amakhalanso ndi mphamvu zoponya munthu mʼGehena.*+ Ndithu ndikukuuzani, muziopa Ameneyu.+