Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi amene uyenera kumuona kuti ndi woyera,+

      Ndi amene uyenera kumuopa,

      Ndipo ndi amene uyenera kumulemekeza.”+

  • Aheberi 10:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kupatsidwa chilango ndi Mulungu wamoyo nʼkoopsa.

  • 1 Petulo 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Muzilemekeza anthu amitundu yonse.+ Muzikonda gulu lonse la abale,+ muziopa Mulungu+ komanso muzilemekeza mfumu.+

  • Chivumbulutso 14:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iye ankanena mofuula kuti: “Opani Mulungu ndi kumupatsa ulemerero chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Choncho lambirani Iye amene anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja+ ndi akasupe amadzi.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena