Yesaya 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wa makamu ndi amene muyenera kumuona kuti ndi woyera,+ ndipo iyeyo ndi amene muyenera kumuopa.+ Iye ndi amene ayenera kukuchititsani kunjenjemera.”+ 1 Petulo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Lemekezani anthu, kaya akhale amtundu wotani.+ Kondani gulu lonse la abale,+ opani Mulungu,+ lemekezani mfumu.+ Chivumbulutso 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anali kunena mofuula kuti: “Opani Mulungu+ ndi kumupatsa ulemerero,+ chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Chotero lambirani Iye amene anapanga+ kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi akasupe amadzi.”+
13 Yehova wa makamu ndi amene muyenera kumuona kuti ndi woyera,+ ndipo iyeyo ndi amene muyenera kumuopa.+ Iye ndi amene ayenera kukuchititsani kunjenjemera.”+
17 Lemekezani anthu, kaya akhale amtundu wotani.+ Kondani gulu lonse la abale,+ opani Mulungu,+ lemekezani mfumu.+
7 Iye anali kunena mofuula kuti: “Opani Mulungu+ ndi kumupatsa ulemerero,+ chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Chotero lambirani Iye amene anapanga+ kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi akasupe amadzi.”+