Yesaya 66:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Iwo adzapita kukaona mitembo ya anthu amene anali kuphwanya malamulo anga,+ pakuti mphutsi zodya mitemboyo sizidzafa. Moto woinyeketsa sudzazima+ ndipo idzakhala chinthu chonyansa kwa anthu onse.”+ Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+
24 “Iwo adzapita kukaona mitembo ya anthu amene anali kuphwanya malamulo anga,+ pakuti mphutsi zodya mitemboyo sizidzafa. Moto woinyeketsa sudzazima+ ndipo idzakhala chinthu chonyansa kwa anthu onse.”+
28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+