Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kunyada kwako kwatsikira ku Manda limodzi ndi phokoso la zoimbira zako za zingwe.+ Mphutsi zayalana pansi pako ngati bedi, ndipo nyongolotsi zasanduka chofunda chako.’+

  • Yesaya 34:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usana ndi usiku, motowo sudzazima. Utsi wake uzidzakwera m’mwamba mpaka kalekale.+ Dzikolo lidzakhala louma ku mibadwomibadwo.+ Mpaka muyaya palibe amene adzadutseko.+

  • Mateyu 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake, ndipo malo ake opunthirapo mbewu adzawayeretseratu kuti mbee! Tirigu adzamututira m’nkhokwe,+ koma mankhusu adzawatentha+ ndi moto umene sungazimitsidwe.”

  • Mateyu 25:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 “Kenako adzauza a kumanzere kwake kuti, ‘Chokani pamaso panga+ inu otembereredwa. Pitani kumoto wosatha+ wokolezedwera Mdyerekezi ndi angelo ake.+

  • Maliko 9:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 kumene mphutsi za mitembo sizifa ndipo moto wake suzima.+

  • 2 Atesalonika 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena