2 Petulo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amenewa ndi akasupe opanda madzi,+ ndi nkhungu yotengeka ndi mphepo yamkuntho, ndipo anawasungira mdima wandiweyani.+ 2 Petulo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo mwa mawu amodzimodziwo, kumwamba+ kumene kulipo panopa limodzi ndi dziko lapansi,+ azisungira moto+ m’tsiku lachiweruzo+ ndi chiwonongeko cha anthu osaopa Mulungu.+
17 Amenewa ndi akasupe opanda madzi,+ ndi nkhungu yotengeka ndi mphepo yamkuntho, ndipo anawasungira mdima wandiweyani.+
7 Ndipo mwa mawu amodzimodziwo, kumwamba+ kumene kulipo panopa limodzi ndi dziko lapansi,+ azisungira moto+ m’tsiku lachiweruzo+ ndi chiwonongeko cha anthu osaopa Mulungu.+