Hagai 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Uza Zerubabele bwanamkubwa wa Yuda kuti,+ ‘Ine ndigwedeza kumwamba ndi dziko lapansi.+ Chivumbulutso 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ iye wotchedwa Mdyerekezi+ ndi Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu. Iye anaponyedwa kudziko lapansi,+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.
9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ iye wotchedwa Mdyerekezi+ ndi Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu. Iye anaponyedwa kudziko lapansi,+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.