Deuteronomo 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 koma wobwezera munthu wodana ndi Mulunguyo mwa kumuwononga+ pamasom’pamaso. Sadzazengereza kuwononga munthu amene amadana ndi Mulungu. Adzam’bwezera pamasom’pamaso. Yesaya 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala kuti adzaimbe mlandu anthu okhala m’dzikoli.+ Magazi amene dzikoli linakhetsa lidzawaonetsa poyera,+ ndipo silidzabisanso anthu amene linapha.”+
10 koma wobwezera munthu wodana ndi Mulunguyo mwa kumuwononga+ pamasom’pamaso. Sadzazengereza kuwononga munthu amene amadana ndi Mulungu. Adzam’bwezera pamasom’pamaso.
21 Pakuti taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala kuti adzaimbe mlandu anthu okhala m’dzikoli.+ Magazi amene dzikoli linakhetsa lidzawaonetsa poyera,+ ndipo silidzabisanso anthu amene linapha.”+