Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mudzawakhalitsa ngati oponyedwa mung’anjo yamoto pa nthawi ya kuonekera kwanu.+

      Yehova adzawameza mu mkwiyo wake, ndipo moto udzawanyeketsa.+

  • Salimo 68:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Monga mmene mphepo imauluzira utsi, inunso muwauluze chimodzimodzi.+

      Ngati mmene phula limasungunukira chifukwa cha moto,+

      Anthu oipa awonongeke ndi kuchotsedwa pamaso pa Mulungu.+

  • Miyambo 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma oipa adzachotsedwa padziko lapansi+ ndipo achinyengo adzazulidwamo.+

  • Yesaya 59:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Iye adzawapatsa mphoto mogwirizana ndi zochita zawo.+ Adani ake adzawapatsa mkwiyo ndipo anthu otsutsana naye adzawapatsa chilango chowayenerera.+ Zilumbanso adzazipatsa chilango choyenerera.+

  • Nahumu 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+

  • 2 Petulo 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndipo mwa mawu amodzimodziwo, kumwamba+ kumene kulipo panopa limodzi ndi dziko lapansi,+ azisungira moto+ m’tsiku lachiweruzo+ ndi chiwonongeko cha anthu osaopa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena