Yesaya 41:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Zilumba inu,+ mvetserani mawu anga mutakhala chete, ndipo mitundu ya anthu+ ipezenso mphamvu. Ibwere pafupi,+ kenako ilankhule. Anthu inu bwerani kufupi nane kumalo oweruzira mlandu.+ Yesaya 41:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zilumba+ zinaona n’kuyamba kuopa. Malekezero a dziko lapansi anayamba kunjenjemera.+ Mitundu ya anthu inasonkhana pamodzi n’kumangobwerabe.
41 “Zilumba inu,+ mvetserani mawu anga mutakhala chete, ndipo mitundu ya anthu+ ipezenso mphamvu. Ibwere pafupi,+ kenako ilankhule. Anthu inu bwerani kufupi nane kumalo oweruzira mlandu.+
5 Zilumba+ zinaona n’kuyamba kuopa. Malekezero a dziko lapansi anayamba kunjenjemera.+ Mitundu ya anthu inasonkhana pamodzi n’kumangobwerabe.