2 Atesalonika 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango cha chiwonongeko chamuyaya+ ndipo adzachotsedwa pamaso pa Ambuye moti sadzaonanso mphamvu zake zaulemerero. 2 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Nsanja ya Olonda,5/1/1989, tsa. 19 Kukambitsirana, tsa. 147
9 Anthu amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango cha chiwonongeko chamuyaya+ ndipo adzachotsedwa pamaso pa Ambuye moti sadzaonanso mphamvu zake zaulemerero.