Yesaya 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kuti iye abisale m’mayenje a m’matanthwe ndi m’ming’alu ya m’miyala ikuluikulu. Adzachita zimenezi chifukwa cha kuopsa kwa Yehova, ndiponso chifukwa cha ulemerero ndi ukulu wake,+ Mulunguyo akadzaimirira kuti dziko lapansi linjenjemere.
21 kuti iye abisale m’mayenje a m’matanthwe ndi m’ming’alu ya m’miyala ikuluikulu. Adzachita zimenezi chifukwa cha kuopsa kwa Yehova, ndiponso chifukwa cha ulemerero ndi ukulu wake,+ Mulunguyo akadzaimirira kuti dziko lapansi linjenjemere.