1 Mbiri 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola,+ ulemerero,+ ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi za padziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu+ ndi wanu, inu Yehova, ndinunso Wokwezeka monga mutu pa onse.+ Salimo 96:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ulemu ndi ulemerero zili pamaso pake.+Mphamvu ndi kukongola zili m’nyumba yake yopatulika.+ Salimo 119:120 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+
11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola,+ ulemerero,+ ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi za padziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu+ ndi wanu, inu Yehova, ndinunso Wokwezeka monga mutu pa onse.+
120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+