Salimo 58:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+ Ezekieli 39:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kwa miyezi 7, a nyumba ya Isiraeli adzakhala akuika m’manda Gogi ndi khamu lake kuti ayeretse dzikolo.+
10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+
12 Kwa miyezi 7, a nyumba ya Isiraeli adzakhala akuika m’manda Gogi ndi khamu lake kuti ayeretse dzikolo.+