Yesaya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tulukani m’Babulo anthu inu!+ Thawani m’manja mwa Akasidi.+ Nenani zimenezi ndi mfuu yachisangalalo kuti zimveke.+ Zineneni mokuwa mpaka zimveke kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+ Yeremiya 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Thawani m’Babulo ndipo tulukani m’dziko la Akasidi.+ Mukhale ngati mbuzi zamphongo ndi nkhosa zamphongo zimene zikutsogolera gulu lonse.+ 2 Akorinto 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Choncho tulukani pakati pawo, lekanani nawo,’ watero Yehova.* ‘Musakhudze chinthu chodetsedwa,’”+ “‘ndipo ndidzakulandirani.’”+ Chivumbulutso 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.
20 Tulukani m’Babulo anthu inu!+ Thawani m’manja mwa Akasidi.+ Nenani zimenezi ndi mfuu yachisangalalo kuti zimveke.+ Zineneni mokuwa mpaka zimveke kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+
8 “Thawani m’Babulo ndipo tulukani m’dziko la Akasidi.+ Mukhale ngati mbuzi zamphongo ndi nkhosa zamphongo zimene zikutsogolera gulu lonse.+
17 “‘Choncho tulukani pakati pawo, lekanani nawo,’ watero Yehova.* ‘Musakhudze chinthu chodetsedwa,’”+ “‘ndipo ndidzakulandirani.’”+
4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.