Yesaya 52:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tembenukani! Tembenukani! Tulukani mmenemo!+ Musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa.+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera, inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+ Yeremiya 51:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ndipo aliyense wa inu apulumutse moyo wake+ ku mkwiyo wa Yehova woyaka moto.+ Chivumbulutso 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.
11 Tembenukani! Tembenukani! Tulukani mmenemo!+ Musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa.+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera, inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+
45 “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ndipo aliyense wa inu apulumutse moyo wake+ ku mkwiyo wa Yehova woyaka moto.+
4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.