Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+

  • Ekisodo 18:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yetero anasangalala kwambiri atamva zabwino zonse zimene Yehova anachitira Aisiraeli powalanditsa m’manja mwa Aiguputo.+

  • Ekisodo 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pamenepo Yetero, apongozi ake a Mose, anabweretsa* nsembe yopsereza ndi nsembe zina kwa Mulungu.+ Ndipo Aroni ndi akulu onse a Isiraeli anabwera n’kudyera limodzi mkate ndi apongozi ake a Mose, pamaso pa Mulungu woona.+

  • Numeri 10:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndiyeno Mose anauza Hobabu yemwe anali mwana wa Reueli+ Mmidiyani, mpongozi wake kuti: “Tikusamukira kumalo amene Yehova anati, ‘Ndidzawapereka kwa inu.’+ Tiyeni tipite limodzi, ndipo tidzakuchitirani zabwino ndithu,+ pakuti Yehova analonjeza Aisiraeli zabwino.”+

  • Aheberi 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena