Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno atsikanawo atafika kunyumba kwa bambo wawo Reueli,+ iye anadabwa ndipo anati: “Bwanji mwabwerako mwamsanga chonchi lero?”

  • Ekisodo 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano Mose anakhala m’busa wa ziweto za Yetero,*+ wansembe wa ku Midiyani, amene anali apongozi ake.+ Pamene anali kuweta ziwetozo chakumadzulo kwa chipululu, anafika kuphiri la Mulungu woona,+ ku Horebe.+

  • Ekisodo 18:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Tsopano Yetero, wansembe wa ku Midiyani, apongozi ake a Mose,+ anamva zonse zimene Mulungu anachitira Mose ndi Aisiraeli, anthu a Mulungu, ndi mmene Yehova anawatulutsira ku Iguputo.+

  • Ekisodo 18:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako Mose anaperekeza apongozi ake+ ndi kutsanzikana nawo, ndipo iwo anabwerera kwawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena