Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno ana a munthu wa mtundu wachikeni,+ amene anali apongozi ake a Mose,+ anatuluka mumzinda wa mitengo ya kanjedza+ pamodzi ndi ana a Yuda kukalowa m’chipululu cha Yuda, chimene chili kum’mwera kwa Aradi.+ Motero iwo anayamba kukhala pamodzi ndi anthuwo.+

  • Oweruza 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Zili choncho, Hiberi+ Mkeni anapatukana ndi Akeni,+ ana a Hobabu mpongozi wa Mose,+ ndipo anamanga hema wake pafupi ndi mtengo waukulu ku Zaananimu, ku Kedesi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena