-
2 Mbiri 28:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako amuna amene anachita kusankhidwa powatchula mayina+ ananyamuka n’kutenga anthu ogwidwawo. Anthu onse amene sanavale* zovala anawaveka zovala+ zimene anafunkha ndipo anawavekanso nsapato. Anawapatsa chakudya+ ndi zakumwa,+ ndipo anawadzoza mafuta. Kuwonjezera apo, aliyense amene anali kuyenda movutikira anamukweza+ pabulu. Atatero anatenga anthuwo n’kupita nawo ku Yeriko,+ kumzinda wa mitengo ya kanjedza,+ kufupi ndi abale awo. Pambuyo pake iwo anabwerera ku Samariya.+
-