Deuteronomo 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anamuonetsa Negebu+ ndi Chigawo+ cha Yorodano kuphatikizapo chigwa cha Yeriko, mzinda wa mitengo ya kanjedza, mpaka ku Zowari.+
3 Anamuonetsa Negebu+ ndi Chigawo+ cha Yorodano kuphatikizapo chigwa cha Yeriko, mzinda wa mitengo ya kanjedza, mpaka ku Zowari.+