Deuteronomo 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anamuonetsa Negebu+ ndi Chigawo*+ cha Yorodano, chigwa cha ku Yeriko, mzinda wa mitengo ya kanjedza,+ mpaka ku Zowari.+
3 Anamuonetsa Negebu+ ndi Chigawo*+ cha Yorodano, chigwa cha ku Yeriko, mzinda wa mitengo ya kanjedza,+ mpaka ku Zowari.+