Genesis 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tiye, fulumira! Thawira kumeneko, ndipo sindichita kanthu mpaka utafika kumeneko.”+ N’chifukwa chake iye anatcha mzindawo dzina lakuti Zowari.*+ Yesaya 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtima wanga ukulirira Mowabu.+ Anthu ake athawira kutali, ku Zowari+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Aliyense akumakwera mtunda wa Luhiti+ akulira. Panjira yopita ku Horonaimu,+ iwo akufuula kwambiri chifukwa cha tsokalo.
22 Tiye, fulumira! Thawira kumeneko, ndipo sindichita kanthu mpaka utafika kumeneko.”+ N’chifukwa chake iye anatcha mzindawo dzina lakuti Zowari.*+
5 Mtima wanga ukulirira Mowabu.+ Anthu ake athawira kutali, ku Zowari+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Aliyense akumakwera mtunda wa Luhiti+ akulira. Panjira yopita ku Horonaimu,+ iwo akufuula kwambiri chifukwa cha tsokalo.