Genesis 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mafumuwa anachita nkhondo ndi mafumu otsatirawa: Bera mfumu ya ku Sodomu,+ Birisa mfumu ya ku Gomora,+ Sinabi mfumu ya ku Adima,+ Semebere mfumu ya ku Zeboyimu,+ ndi mfumu ya ku Bela (kapena kuti ku Zowari).+
2 mafumuwa anachita nkhondo ndi mafumu otsatirawa: Bera mfumu ya ku Sodomu,+ Birisa mfumu ya ku Gomora,+ Sinabi mfumu ya ku Adima,+ Semebere mfumu ya ku Zeboyimu,+ ndi mfumu ya ku Bela (kapena kuti ku Zowari).+