19 Choncho malire a dziko la Akanani anachokera ku Sidoni mpaka ku Gerari+ kufupi ndi Gaza,+ n’kukafika ku Sodomu ndi Gomora+ mpakanso ku Adima+ ndi Zeboyimu,+ kufupi ndi Lasa.
12 Abulamu anakakhala kudziko la Kanani, koma Loti anakakhala pakati pa mizinda ya m’Chigawocho.+ Potsirizira pake, anakamanga hema wake pafupi ndi Sodomu.
6 Anaweruzanso mizinda ya Sodomu ndi Gomora mwa kuinyeketsa ndi moto,+ kuti chikhale chitsanzo cha zinthu zimene zidzachitikire anthu osaopa Mulungu m’tsogolo.+