Genesis 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho pamene Mulungu anawononga mizinda ya m’Chigawocho, anakumbukira Abulahamu. Anatero mwa kupulumutsa Loti ku chiwonongeko pamene ankawononga mizinda imene Loti anali kukhalako.+
29 Choncho pamene Mulungu anawononga mizinda ya m’Chigawocho, anakumbukira Abulahamu. Anatero mwa kupulumutsa Loti ku chiwonongeko pamene ankawononga mizinda imene Loti anali kukhalako.+