8 Pa nthawi imeneyi, mfumu ya ku Sodomu, mfumu ya ku Gomora, mfumu ya ku Adima, mfumu ya ku Zeboyimu, ndi mfumu ya ku Bela (kapena kuti ku Zowari), ananyamuka n’kutsetserekera kuchigwa cha Sidimu.+ Kumeneko, iwo anafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo kuti amenyane ndi