Yesaya 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtima wanga ukulirira Mowabu. Anthu ake athawira kutali, ku Zowari+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Iwo akulira pamene akukwera mtunda wa Luhiti.Panjira yopita ku Horonaimu, iwo akulira kwambiri chifukwa cha tsokalo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:5 Yesaya 1, tsa. 193
5 Mtima wanga ukulirira Mowabu. Anthu ake athawira kutali, ku Zowari+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Iwo akulira pamene akukwera mtunda wa Luhiti.Panjira yopita ku Horonaimu, iwo akulira kwambiri chifukwa cha tsokalo.+