Yeremiya 48:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “‘Kulira kochokera ku Hesiboni+ kukumveka ku Eleyale.+ Kulira kwawo kukumveka mpaka ku Yahazi,+Kukumveka kuchokera ku Zowari kukafika ku Horonaimu+ ndi ku Egilati-selisiya. Ngakhale madzi a ku Nimurimu adzauma.+
34 “‘Kulira kochokera ku Hesiboni+ kukumveka ku Eleyale.+ Kulira kwawo kukumveka mpaka ku Yahazi,+Kukumveka kuchokera ku Zowari kukafika ku Horonaimu+ ndi ku Egilati-selisiya. Ngakhale madzi a ku Nimurimu adzauma.+