Yeremiya 48:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ku Horonaimu+ kwamveka kulira kofuula,Kwamveka phokoso lachiwonongeko ndi kugwa kwakukulu. Yeremiya 48:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu akulira mosalekeza pamene akukwera zitunda za Luhiti. Ndipo panjira yochokera ku Horonaimu akumva anthu akulira mowawidwa mtima chifukwa cha tsoka limene lawagwera.+
5 Anthu akulira mosalekeza pamene akukwera zitunda za Luhiti. Ndipo panjira yochokera ku Horonaimu akumva anthu akulira mowawidwa mtima chifukwa cha tsoka limene lawagwera.+