Yesaya 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtima wanga ukulirira Mowabu. Anthu ake athawira kutali, ku Zowari+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Iwo akulira pamene akukwera mtunda wa Luhiti.Panjira yopita ku Horonaimu, iwo akulira kwambiri chifukwa cha tsokalo.+ Yeremiya 48:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “‘Kulira kochokera ku Hesiboni+ kukumveka ku Eleyale.+ Kulira kwawo kukumveka mpaka ku Yahazi,+Kukumveka kuchokera ku Zowari kukafika ku Horonaimu+ ndi ku Egilati-selisiya. Ngakhale madzi a ku Nimurimu adzauma.+
5 Mtima wanga ukulirira Mowabu. Anthu ake athawira kutali, ku Zowari+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Iwo akulira pamene akukwera mtunda wa Luhiti.Panjira yopita ku Horonaimu, iwo akulira kwambiri chifukwa cha tsokalo.+
34 “‘Kulira kochokera ku Hesiboni+ kukumveka ku Eleyale.+ Kulira kwawo kukumveka mpaka ku Yahazi,+Kukumveka kuchokera ku Zowari kukafika ku Horonaimu+ ndi ku Egilati-selisiya. Ngakhale madzi a ku Nimurimu adzauma.+